Yoswa 24:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anthu anayankha, nati, Sikungatheke kuti timsiye Yehova, ndi kutumikira milungu yina;

Yoswa 24

Yoswa 24:15-24