Yoswa 24:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinatuma mabvu atsogolere inu, amene anawaingitsa pamaso panu, ndiwo mafumu awiri a Aamori; osati ndi lupanga lako, kapena ndi uta wako ai.

Yoswa 24

Yoswa 24:7-17