Yoswa 23:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

osalowa pakati pa amitundu awa otsala mwa inu; kapena kuchula dzina la milungu yao; osalumbiritsa nalo, kapena kuitumikira, kapena kuigwadira;

Yoswa 23

Yoswa 23:3-11