Yoswa 23:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kudzakhala kuti monga zakugwerani zokoma zonse anakunenerani Yehova Mulungu wanu, momwemo Yehova adzakutengerani zoipa zonse mpaka atakuonongani kukucotsani m'dziko lokoma ili anakupatsani Yehova Mulungu wanu.

Yoswa 23

Yoswa 23:8-16