Yoswa 23:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Munthu mmodzi wa inu adzapitikitsa anthu cikwi cimodzi; pakuti Yehova Mulungu wanu ndiye amathirira inu nkhondo monga ananena ndi inu.

Yoswa 23

Yoswa 23:1-12