Yoswa 21:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ana a Israyeli anapatsa Alevi, kutapa pa colowa cao, monga mwa lamulo la Yehova, midzi iyi ndi mabusa ao.

Yoswa 21

Yoswa 21:1-4