Yoswa 21:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kwa ana a Aroni wansembe anapatsa Hebroni ndi mabusa ace, ndiwo mudzi wopulumukirako wakupha mnzace, ndi Libina ndi mabusa ace;

Yoswa 21

Yoswa 21:11-15