Yoswa 20:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Munthu akathawira umodzi wa midzi iyi, aziima polowera pa cipata ca mudziwo, nafotokozere mlandu wace m'makutu a akuru a mudziwo; pamenepo azimlandira kumudzi kwao, ndi kumpatsa malo, kuti akhale pakati pao.

Yoswa 20

Yoswa 20:1-9