Yoswa 2:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo amunawo anawalondola pa njira ya ku Yordano yomka kudooko; ndipo ataturuka akuwalondola, anatseka pacipata.

Yoswa 2

Yoswa 2:6-14