Yoswa 2:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma mkaziyo anatenga amuna awiriwo, nawabisa; natero, Inde, amunawo anandifikira; koma sindinadziwa uko afuma;

Yoswa 2

Yoswa 2:1-10