Yoswa 19:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

M'gawo la ana a Yuda muli colowa ca ana a Simeoni; popeza gawo la ana a Yuda linawacurukira; cifukwa cace ana a Simeoni anali naco colowa pakati pa colowa coo.

Yoswa 19

Yoswa 19:6-14