Yoswa 19:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

nazungulira malice kumka ku Rama, ndi ku mudzi wa linga la Turo; nazungulira malire kumka ku Hosa; ndi maturukiro ace anali kunyanja, kucokera ku Hebeli mpaka ku Akizibu;

Yoswa 19

Yoswa 19:28-38