Yoswa 18:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mudzifunire amuna, pfuko liri lonse amuna atatu; kuti ndiwatume, anyamuke, nayendeyende iwo pakati pa dziko, nalilembe monga mwa colowa cao; nabwereoso kwa ine.

Yoswa 18

Yoswa 18:1-11