26. ndi Mizipe, ndi Kefira, ndi Moza;
27. ndi Rekemu, ndi Iripeeli ndi Tarala;
28. ndi Zela, Elefi, ndi Yebusi, womwewo ndi Yerusalemu, Gibeati ndi Kiriyati; midzi khumi ndi inai pamodzi ndi miraga yace, Ndico colowa ca ana a Benjamini monga mwa mabanja ao.