Yoswa 18:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo maere a ana a Benjamini anakwera monga mwa mabanja ao; ndi malire a gawo lao anaturuka pakati pa ana a Yuda ndi ana a Yosefe.

Yoswa 18

Yoswa 18:5-18