Yoswa 17:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Natsikira malire ku mtsinje wa Kana, kumwera kwa mtsinje; midzi iyi inakhala ya Efraimu pakati pa midzi ya Manase; ndi malire a Manase anali kumpoto kwa mtsinje; ndimaturukiro ace anali kunyanja;

Yoswa 17

Yoswa 17:3-12