Yoswa 17:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo ana a Yosefe ananena ndi Yoswa, ndi kuti, Watipatsiranji colowa cathu camaere cimodzi ndi gawo limodzi, popeza ife ndife anthu aunyinji, pakuti Yehova anatidalitsa ndi pano pomwe?

Yoswa 17

Yoswa 17:5-16