Yoswa 17:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Gawo la pfuko la Manase ndi ili: pakuti anali woyamba wa Yosefe. Makiri mwana woyamba wa Manase, atate wa Gileadi, popeza ndiye munthu wa nkhondo, anakhala nayo Gileadi ndi Basana.

Yoswa 17

Yoswa 17:1-7