Yoswa 16:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kuyambira ku Tapua malire anamuka kumadzulo ku mtsinje wa Kana; ndi maturukiro ace anali kunyanja. Ici ndi colowa ca pfuko la ana a Efraimu monga mwa mabanja ao;

Yoswa 16

Yoswa 16:1-9