Yoswa 16:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo malire a ana a Efraimu, monga mwa mabanja ao, ndiwo: malire a colowa cao kum'mawa ndiwo Atarotu-Adara, mpaka Betihoroni wa kumtunda;

Yoswa 16

Yoswa 16:1-10