Yoswa 16:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

natsikira kumadzulo kumka ku malire a Ayafeleti, ku malire a Beti-horoni wa kunsi, ndi ku Gezeri; ndi maturukiro ace anali kunyanja.

Yoswa 16

Yoswa 16:1-10