Yoswa 15:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

napitirira ku Azimoni, naturuka ku mtsinje wa Aigupto; ndi malekezero a malirewa anali ku Nyanja Yaikuru; awa ndi malire anu a kumwera.

Yoswa 15

Yoswa 15:1-11