Yoswa 14:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo ana a Yuda anadza kwa Yoswa ku Giligala; ndi Kalebe mwana wa Yefune Mkenizi ananena naye, Mudziwa cimene Yehova adanena kwa Mose munthu wa Mulungu za ine ndi za inu m'KadesiBarinea.

Yoswa 14

Yoswa 14:1-12