Yoswa 14:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma lero lino ndiri wamphamvu monga tsiku lija anandituma Mose; monga mphamvu yanga pamene paja, momwemo mphamvu yanga tsopano, kugwira nkhondo, ndi kuturuka ndi kulowa.

Yoswa 14

Yoswa 14:4-14