Yoswa 13:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mose anaperekanso colowa kwa pfuko la Manase logawika pakati, ndico ca pfuko la Manase logawika pakati monga mwa mabanja ao.

Yoswa 13

Yoswa 13:25-33