Yoswa 12:23-24 Buku Lopatulika 1992 (BL92) mfumuya ku Doro, mpaka ponyamuka pa Doro, imodzi; mfumu ya ku Goimu m'Giligala, imodzi; mfumu ya ku Tiriza, imodzi