Yoswa 12:16-20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

16. mfumu ya ku Makeda, imodzi; mfumu ya ku Beteli, imodzi;

17. mfumu ya ku Tapuwa, imodzi; mfumu ya ku Heferi, imodzi;

18. mfumu ya ku Afeki, imodzi; mfumu ya ku Lasaroni, imodzi;

19. mfumu ya ku Madoni, imodzi; mfumu ya ku Hazori, imodzi;

20. mfumu ya ku Simironi-meroni, imodzi; mfumu ya ku Akasafu, imodzi;

Yoswa 12