Yoswa 11:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anaturuka, iwo ndi makamu ao onse nao, anthu ambiri, kucuruka kwao ngati mcenga uli m'mphepete mwa nyanja; ndi akavalo ndi magareta ambirimbiri.

Yoswa 11

Yoswa 11:3-7