Yoswa 11:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yoswa anabwerera m'mbuyo nthawi imeneyi nalanda Hazori nakantha mfumu yace ndi lupanga; pakuti kale Hazori unali waukuru wa maufumu aja onse.

Yoswa 11

Yoswa 11:1-17