Yoswa 10:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

anaopa kwambiri, popeza Gibeoni ndi mudzi waukuru, monga wina wa midzi yacifumu, popezanso unaposa Ai kukula kwace, ndi amuna ace onse ndiwo amphamvu.

Yoswa 10

Yoswa 10:1-12