Yoswa 1:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Palibe munthu adzatha kuima pamaso pako masiku onse a moyo wako; monga ndinakhala ndi Mose momwemo ndidzakhala ndi iwe; sindidzakusowa, sindidzakusiya.

Yoswa 1

Yoswa 1:3-15