Yoswa 1:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kumbukilani mau amene Mose mtumiki wa Yehova anakulamulirani inu, kuti, Yehova Mulungu wanu akupatsani mpumulo, nadzakupatsani dziko lino.

Yoswa 1

Yoswa 1:11-18