Yohane 9:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo akuphunzira ace anamfunsa iye, nanena, Rabi, anacimwa ndani, ameneyo, kapena atate wace ndi amace, kuti anabadwa wosaona?

Yohane 9

Yohane 9:1-11