Yohane 9:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace Ayuda sanakhulupirira za iye, kuti anali wosaona, napenya, kufikira kumene adaitana atate wace ndi amace a iye wopenya;

Yohane 9

Yohane 9:13-21