Yohane 8:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Koma Yesu anamuka ku phiri la Azitona.

2. Komac mamawa anadzanso kuKacisi, ndipo anthu onse anadza kwa iye; ndipo m'mene anakhala pansi anawaphunzitsa.

Yohane 8