Yohane 7:52-53 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

52. Anayankha nati kwa iye, Kodi iwenso uli woturuka m'Galileya? Santhula, nuone kuti m'Galileya sanauka mneneri.

53. Ndipo anamuka munthu yense ku nyumba yace.

Yohane 7