Yohane 7:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma ambiri a m'khamu la anthu anakhulupirira iye; ndipo ananena, Pamene Kristu akadza kodi adzacita zizindikilo zambiri zoposa zimene adazicita ameneyo?

Yohane 7

Yohane 7:22-41