Yohane 7:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace abale ace anati kwa iye, Cokani pano, mumuke ku Yudeya, kuti akuphunzita anunso akapenye nchito zanu zimenemucita.

Yohane 7

Yohane 7:1-12