Yohane 7:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ngati munthu ali yense afuna kucita cifuniro cace, adzazindikira za ciphunzitsoco, ngati cicokera kwa Mulungu, kapena ndilankhula zocokera kwa Ine ndekha.

Yohane 7

Yohane 7:14-27