Yohane 7:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo zitapita izi Yesu anayendayenda m'Galileya; pakuti sanafuna kuyendayenda m'Yudeya, cifukwa Ayuda anafuna kumupha iye.

Yohane 7

Yohane 7:1-10