Yohane 6:61 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Yesu podziwa mwa yekha kuti akuphunzira ace alikung'ung'udza cifukwa ca ici, anati kwa iwo, ici mukhumudwa naco?

Yohane 6

Yohane 6:55-69