Yohane 6:37 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cinthu conse cimene anandipatsa Ine Atate cidzadza kwa Ine; ndipo wakudza kwa Ine sindidzamtaya iye kunja.

Yohane 6

Yohane 6:31-47