Yohane 6:32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace Yesu anati kwa iwo, Indetu, indetu, ndinena kwa inu, Si Mose amene anakupatsani inu mkate wa Kumwamba; koma Atate wanga akupatsani inu mkate woona wa Kumwamba.

Yohane 6

Yohane 6:26-36