Yohane 6:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

cifukwa cace pamene khamu la anthu linaona kuti palibe Yesu, ndi akuphunzira ace palibe, iwo okha analowa m'ngalawazo nadza ku Kapernao, alikufuna Yesu.

Yohane 6

Yohane 6:17-25