Yohane 5:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yesu, pakuona ameneyo alikugona, ndipo anadziwa kuti anatero nthawi yaikuru pamenepo, ananena naye, Ufuna kuciritsidwa kodi?

Yohane 5

Yohane 5:2-7