Yohane 5:32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Wocita umboni wa Ine ndi wina; ndipo ndidziwa kuti umboni umene iye andicitira Ine uli woona.

Yohane 5

Yohane 5:27-42