Yohane 5:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Sindikhoza kucita kanthu kwa Ine ndekha; monga momwe ndimva ndiweruza; ndipo maweruzidwe anga ali olungama; cifukwa kuti sinditsata cifuniro canga, koma cifuniro ca Iye ondituma Ine.

Yohane 5

Yohane 5:27-34