Yohane 5:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Indetu, indetu, ndinena kwa inu, kuti iye wakumva mau anga, ndi kukhulupirira iye amene anandituma Ine, ali nao moyo wosatha, ndipo salowa m'kuweruza, koma wacokera kuimfa, nalowa m'moyo.

Yohane 5

Yohane 5:17-26