Yohane 5:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti Atate akonda Mwana, namuonetsa zonse azicita yekha: ndipo adzamuonetsa nchito zoposa izi, kuti mukazizwe,

Yohane 5

Yohane 5:19-21