Yohane 5:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma wociritsidwayo sanadziwa ngati ndani; pakuti Yesu anacoka kacetecete, popeza panali anthu aunyinji m'malo muja.

Yohane 5

Yohane 5:11-20